Sembe umoyo ogula
Sembe kuliye kuti tinalinawo
Eti siya
Mwana wanga
Ziko la vuta
Antu nawo alimba mutima
Matenda nayo
Siyo sila
Mwana wanga
Ziko la vuta
Antu nawo alimba mutima
Matenda nayo
Siyo sila
Nizaku wuza bwanji
Kuti umve
Kuti umvele
Mwana
Nizakuwuza bwanji
Kuti umve
Kuti umvele
Mwana
Mwanaaa
## CHORUS
Mvela mvela mvel...
Comments