## VERSE 1
Pa ziko latu palibe cha bwino
Bantu ba kungoni mvelela ma jealousy
(Ma jealousy)
Ba kungo funsa
Achita chani
Ali na ndani
Kodi ni bwanji
Sungazi nkalile chabe weka iwe
(Ni ma yesa)
Ku sekelela chalo chonse
(Ni ma yesa)
Ku tandiza chalo chonse eh
(Chi ma kanga)
Ku konda we saku konda weh
Mulungu wanga
Ni tandizeni
Sinifuno chimwa oh wo
## CHORUS
Amb...
Comments